Link to home pageLanguagesLink to all Bible versions on this site
Salimo 117
1 Tamandani Yehova, inu anthu a mitundu yonse;
mulemekezeni Iye, inu mitundu ya anthu.
2 Pakuti chikondi chake pa ife ndi chachikulu,
ndipo kukhulupirika kwa Yehova nʼkosatha.
 
Tamandani Yehova.

<- MASALIMO 116MASALIMO 118 ->